Numeri 29:5 - Buku Lopatulika ndi tonde mmodzi wa nsembe yauchimo, yakutetezera inu; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi tonde mmodzi wa nsembe yauchimo, yakutetezera inu; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Muperekenso tonde mmodzi kuti akhale nsembe yochitira mwambo wopepesera machimo anu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Muziperekanso mbuzi yayimuna kuti izikhala nsembe yopepesera machimo anu. |
Ndi tonde mmodzi, akhale nsembe yauchimo ya Yehova; aikonze pamodzi ndi nsembe yopsereza yosalekeza, ndi nsembe yake yothira.
ndi limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi, momwemo ndi anaankhosa asanu ndi awiri;
pamodzi ndi nsembe yopsereza ya pamwezi, ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe yopsereza yosalekeza, ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira, monga mwa lemba lake, zikhale za fungo lokoma, nsembe yamoto ya Yehova.