ndi nsembe yake ya efa wa ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta, atatu a magawo khumi akhale a ng'ombe imodzi, awiri a magawo khumi akhale a nkhosa yamphongo imodzi,
Numeri 28:29 - Buku Lopatulika limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi, momwemo ndi anaankhosa asanu ndi awiri; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi, momwemo ndi anaankhosa asanu ndi awiri; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa ndiponso wa kilogaramu limodzi pa mwanawankhosa aliyense. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo pa mwana wankhosa aliyense mwa asanu ndi awiri aja, kilogalamu imodzi. |
ndi nsembe yake ya efa wa ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta, atatu a magawo khumi akhale a ng'ombe imodzi, awiri a magawo khumi akhale a nkhosa yamphongo imodzi,