ndi nsembe yao ya efa wa ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta; mupereke atatu a magawo khumi akhale a ng'ombe, ndi awiri a magawo khumi akhale a nkhosa yamphongo;
Numeri 28:21 - Buku Lopatulika upereke limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi; uzitero ndi anaankhosa asanu ndi awiri; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 upereke limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi; uzitero ndi anaankhosa asanu ndi awiri; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa ndiponso wa makilogaramu limodzi pa mwanawankhosa aliyense. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kilogalamu imodzi pa mwana wankhosa aliyense mwa ana ankhosa asanu ndi awiri aja. |
ndi nsembe yao ya efa wa ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta; mupereke atatu a magawo khumi akhale a ng'ombe, ndi awiri a magawo khumi akhale a nkhosa yamphongo;