Ndi ana a Efuremu: Sutela, ndi Beredi mwana wake, ndi Tahati mwana wake, ndi Eleada mwana wake, ndi Tahati mwana wake,
Numeri 26:36 - Buku Lopatulika Ndipo mwana wamwamuna wa Sutela ndiye Erani, ndiye kholo la banja la Aerani. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo mwana wamwamuna wa Sutela ndiye Erani, ndiye kholo la banja la Aerani. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndipo ana aamuna a Sutela anali aŵa: Erani anali kholo la banja la Aerani. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Zidzukulu za Sutela zinali izi: kuchokera mwa Erani, fuko la Aerani. |
Ndi ana a Efuremu: Sutela, ndi Beredi mwana wake, ndi Tahati mwana wake, ndi Eleada mwana wake, ndi Tahati mwana wake,
Ana aamuna a Efuremu monga mwa mabanja ao ndiwo: Sutela, ndiye kholo la banja la Asutela; Bekere, ndiye kholo la banja la Abekere; Tahani, ndiye kholo la banja la Atahani.
Iwo ndiwo mabanja a ana a Efuremu monga mwa owerengedwa ao, ndiwo zikwi makumi atatu mphambu ziwiri kudza mazana asanu. Iwo ndiwo ana aamuna a Yosefe monga mwa mabanja ao.