Numeri 23:28 - Buku Lopatulika Ndipo Balaki ananka naye Balamu pamwamba pa Peori, popenyana ndi chipululu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Balaki ananka naye Balamu pamwamba pa Peori, popenyana ndi chipululu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Choncho Balaki adatenga Balamu, napita naye pamwamba pa phiri la Peori loyang'anana ndi chipululu cham'munsi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo Balaki anamutengera Balaamu pamwamba pa Peori, poyangʼanana ndi chipululu. |
atachoka ku Bamoti ku chigwa chili m'dziko la Mowabu, ku mutu wa Pisiga, popenyana ndi chipululu.
Ndipo Balaki anati kwa Balamu, Tiyetu, ndimuke nawe kumalo kwina; kapena kudzakomera pamaso pa Mulungu kuti unditembererere iwo pokhala kumeneko.
Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Mundimangire pano maguwa a nsembe asanu ndi awiri, nimundikonzere pano ng'ombe zisanu ndi ziwiri, ndi nkhosa zamphongo zisanu ndi ziwiri.
Pamene Balamu anaona kuti kudakomera pamaso pa Yehova kudalitsa Israele, sanamuke, monga nthawi zina zija, ku nyanga zolodzera, koma anayang'ana nkhope yake kuchipululu.