Taonani, anthuwo auka ngati mkango waukazi, nadzitukumula ngati mkango waumuna. Sugonanso kufikira utadya nyama yogwira, utamwa mwazi wa zophedwa.
Numeri 23:25 - Buku Lopatulika Ndipo Balaki anati kwa Balamu, Usawatemberera konse, kapena kuwadalitsa konse. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Balaki anati kwa Balamu, Usawatemberera konse, kapena kuwadalitsa konse. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Balaki adauza Balamu kuti, “Musaŵatemberere, ndipo musaŵadalitse.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo Balaki anati kwa Balaamu, “Usawatemberere ndi pangʼono pomwe kapena kuwadalitsa! |
Taonani, anthuwo auka ngati mkango waukazi, nadzitukumula ngati mkango waumuna. Sugonanso kufikira utadya nyama yogwira, utamwa mwazi wa zophedwa.
Koma Balamu anayankha nati kwa Balaki, Sindinakuuzani ndi kuti, Chilichonse achinena Yehova, chomwecho ndizichita?