Ndipo padzakhala kuti pamene Mowabu adzadzionetsa yekha, ndi kudzitopetsa pamsanje, ndipo kufika kumalo ake oyera kudzapemphera, sadzapindulapo kanthu.
Numeri 22:39 - Buku Lopatulika Ndipo Balamu anamuka ndi Balaki, nafika iwo ku Kiriyati-Huzoti. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Balamu anamuka ndi Balaki, nafika iwo ku Kiriyati-Huzoti. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono Balamu adapita limodzi ndi Balaki, nakafika ku Kiriyati-Huzoti. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamenepo Balaamu anapita pamodzi ndi Balaki ku Kiriati-Huzoti. |
Ndipo padzakhala kuti pamene Mowabu adzadzionetsa yekha, ndi kudzitopetsa pamsanje, ndipo kufika kumalo ake oyera kudzapemphera, sadzapindulapo kanthu.
Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Taonani, ndafika kwa inu; ngati ndili nayo mphamvu konse tsopano kunena kanthu? Mau amene Mulungu aike m'kamwa mwanga ndiwo ndidzanena.
Pamenepo Balaki anapha ng'ombe ndi nkhosa, natumizira Balamu, ndi akalonga okhala naye.