Numeri 21:31 - Buku Lopatulika Chomwecho Israele anakhala m'dziko la Aamori. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Chomwecho Israele anakhala m'dziko la Aamori. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Motero Aisraele adakhala m'dziko la Aamori. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Choncho Aisraeli anakhala mʼdziko la Aamori.” |
Tinawagwetsa; Hesiboni waonongeka kufikira ku Diboni, ndipo tinawapululutsa kufikira ku Nofa. Ndiwo wakufikira ku Medeba.
Ndipo Mose anatumiza anthu akazonde Yazere, nalanda midzi yake, napirikitsa Aamori a komweko.
Ndipo ndinatuma mavu atsogolere inu, amene anawaingitsa pamaso panu, ndiwo mafumu awiri a Aamori; osati ndi lupanga lako, kapena ndi uta wako ai.