Ndipo ana a Israele anachita monga mwa zonse Yehova adauza Mose, momwemo anamanga mahema ao pa mbendera zao, momwemonso anayenda paulendo, yense monga mwa mabanja ake, monga mwa nyumba za makolo ake.
Numeri 2:33 - Buku Lopatulika Koma sanawerenge Alevi mwa ana a Israele; monga Yehova adauza Mose. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma sanawerenge Alevi mwa ana a Israele; monga Yehova adauza Mose. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma Alevi sadaŵaŵerengere kumodzi ndi Aisraele, monga momwe Chauta adaalamulira Mose. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma Alevi sanawawerenge pamodzi ndi Aisraeli enawo monga momwe Yehova analamulira Mose. |
Ndipo ana a Israele anachita monga mwa zonse Yehova adauza Mose, momwemo anamanga mahema ao pa mbendera zao, momwemonso anayenda paulendo, yense monga mwa mabanja ake, monga mwa nyumba za makolo ake.