Numeri 16:50 - Buku Lopatulika Ndipo Aroni anabwera kwa Mose ku khomo la chihema chokomanako; ndi mliri unaleka. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Aroni anabwera kwa Mose ku khomo la chihema chokomanako; ndi mliri unaleka. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pambuyo pake Aroni adabwerera kwa Mose ku chipata cha chihema chamsonkhano, mliriwo utaleka. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo Aaroni anabwerera kwa Mose ku khomo la tenti ya msonkhano, chifukwa mliriwo unali utatha. |
Koma akufa nao mliri ndiwo zikwi khumi ndi zinai mphambu mazana asanu ndi awiri, osawerenga aja adafera chija cha Kora.