Ndipo ananena nao, Ichi ndi chomwe Yehova analankhula, Mawa ndiko kupuma, Sabata lopatulika la Yehova; chimene muziotcha, otchani, ndi chimene muziphika phikani; ndi chotsala chikukhalireni chosungika kufikira m'mawa.
Numeri 15:32 - Buku Lopatulika Ndipo pokhala ana a Israele m'chipululu, anapeza munthu wakufuna nkhuni tsiku la Sabata. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo pokhala ana a Israele m'chipululu, anapeza munthu wakufuna nkhuni tsiku la Sabata. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamene Aisraele anali m'chipululu muja, adapeza munthu akutola nkhuni pa tsiku la Sabata. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Aisraeli ali mʼchipululu, munthu wina anapezeka akutola nkhuni tsiku la Sabata. |
Ndipo ananena nao, Ichi ndi chomwe Yehova analankhula, Mawa ndiko kupuma, Sabata lopatulika la Yehova; chimene muziotcha, otchani, ndi chimene muziphika phikani; ndi chotsala chikukhalireni chosungika kufikira m'mawa.
atero Yehova: Tadzayang'anirani nokha, musanyamule katundu tsiku la Sabata, musalowe naye pa zipata za Yerusalemu;
Ndipo amene adampezawo alinkufuna nkhuni anabwera naye kwa Mose ndi Aroni, ndi kwa khamu lonse.