Numeri 14:38 - Buku Lopatulika Koma Yoswa mwana wa Nuni, ndi Kalebe mwana wa Yefune, anakhala ndi moyo mwa amuna aja adamukawo kukazonda dziko. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma Yoswa mwana wa Nuni, ndi Kalebe mwana wa Yefune, anakhala ndi moyo mwa amuna aja adamukawo kukazonda dziko. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma mwa anthu amene adapita kukazonda dziko aja, Yoswa mwana wa Nuni ndi Kalebe mwana wa Yefune ndiwo adatsala amoyo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mwa anthu amene anakaona dzikolo, Yoswa mwana wa Nuni ndi Kalebe mwana wa Yefune ndi okhawo amene anapulumuka. |
Popeza Yehova adanena za iwowa, Adzafatu m'chipululu. Ndipo sanatsalire mmodzi wa iwowa koma Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.