Numeri 10:26 - Buku Lopatulika Ndi pa gulu la fuko la ana a Asere anayang'anira Pagiyele mwana wa Okarani. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi pa gulu la fuko la ana a Asere anayang'anira Pagiyele mwana wa Okarani. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mtsogoleri wa gulu la fuko la Asere anali Pagiyele mwana wa Okarani. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pagieli mwana wa Okirani ndiye anali mtsogoleri wa fuko la Aseri, |
Pamenepo anayenda a mbendera ya chigono cha ana a Dani, ndiwo a m'mbuyombuyo a zigono zonse, monga mwa magulu ao; ndi pa gulu lake anayang'anira Ahiyezere mwana wa Amisadai.