Nehemiya 9:34 - Buku Lopatulika
ndi mafumu athu, akulu athu, ansembe athu, ndi makolo athu, sanasunge chilamulo chanu, kapena kumvera malamulo anu, ndi mboni zanu, zimene munawachitira umboni nazo.
Onani mutuwo
ndi mafumu athu, akulu athu, ansembe athu, ndi makolo athu, sanasunge chilamulo chanu, kapena kumvera malamulo anu, ndi mboni zanu, zimene munawachitira umboni nazo.
Onani mutuwo
Mafumu athu, akulu athu, ansembe athu ndi makolo athu, sadasunge mau anu, ndipo sadasamale malamulo anu ndi malangizo anu amene mudaŵapatsa.
Onani mutuwo
Ndipotu mafumu athu, atsogoleri athu, ansembe athu ndi makolo athu sanatsatire mawu anu. Iwo sanalabadire za malamulo anu ngakhale mawu anu owachenjeza amene munawapatsa.
Onani mutuwo