Ndi Aisraele a ana a Parosi: Ramiya, ndi Iziya, ndi Matikiya, ndi Miyamini, ndi Eleazara, ndi Malikiya, ndi Benaya.
Nehemiya 7:8 - Buku Lopatulika ana a Parosi zikwi ziwiri mphambu zana limodzi kudza makumi asanu ndi awiri. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ana a Parosi zikwi ziwiri mphambu zana limodzi kudza makumi asanu ndi awiri. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa A banja la Parosi 2,172. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Zidzukulu za Parosi 2,172 |
Ndi Aisraele a ana a Parosi: Ramiya, ndi Iziya, ndi Matikiya, ndi Miyamini, ndi Eleazara, ndi Malikiya, ndi Benaya.
ana a Parosi, zikwi ziwiri ndi zana limodzi mphambu makumi asanu ndi awiri kudza awiri.
Wa ana a Sekaniya, wa ana a Parosi, Zekariya; ndi pamodzi naye, powawerenga monga mwa chibadwidwe chao, amuna zana limodzi mphambu makumi asanu.
ndiwo amene anadza ndi Zerubabele: Yesuwa, Nehemiya, Azariya, Raamiya, Nahamani, Mordekai, Bilisani, Misipereti, Bigivai, Nehumu, Baana. Mawerengedwe a amuna a anthu Aisraele ndiwo: