Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




Nehemiya 7:68 - Buku Lopatulika

Akavalo ao ndiwo mazana asanu ndi awiri mphambu makumi atatu kudza asanu ndi mmodzi; nyuru zao mazana awiri mphambu makumi anai kudza zisanu;

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Akavalo ao ndiwo mazana asanu ndi awiri mphambu makumi atatu kudza asanu ndi mmodzi; nyuru zao mazana awiri mphambu makumi anai kudza zisanu;

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Akavalo ao analipo 736, nyulu zao zinalipo 245,

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Panali akavalo 736, abulu angʼonoangʼono 245.

Onani mutuwo



Nehemiya 7:68
3 Mawu Ofanana  

osawerenga akapolo ao aamuna ndi aakazi, ndiwo zikwi zisanu ndi ziwiri mphambu mazana atatu ndi makumi atatu kudza asanu ndi awiri; ndipo anakhala nao aamuna ndi aakazi oimbira mazana awiri mphambu makumi anai kudza asanu ndi mmodzi.


ngamira zao mazana anai mphambu makumi atatu kudza asanu; abulu ao zikwi zisanu ndi chimodzi mphambu mazana asanu ndi awiri kudza makumi awiri.