a ana a Asafu: Zakuri, ndi Yosefe, ndi Netaniya, ndi Asarela, ana a Asafu; mwa chilangizo cha Asafu, wakunenera mwa chilangizo cha mfumu.
Nehemiya 7:44 - Buku Lopatulika Oimbira: ana a Asafu, zana limodzi mphambu makumi anai kudza asanu ndi atatu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Oimbira: ana a Asafu, zana limodzi mphambu makumi anai kudza asanu ndi atatu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Oimba nyimbo anali aŵa: a banja la Asafu 148. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anthu oyimba: Zidzukulu za Asafu 148. |
a ana a Asafu: Zakuri, ndi Yosefe, ndi Netaniya, ndi Asarela, ana a Asafu; mwa chilangizo cha Asafu, wakunenera mwa chilangizo cha mfumu.
Odikira: ana a Salumu, ana a Atere, ana a Talimoni, ana a Akubu, ana a Hatita, ana a Sobai, zana limodzi mphambu makumi atatu kudza asanu ndi atatu.