Ana a Harimu, chikwi chimodzi mphambu khumi limodzi kudza asanu ndi awiri.
A banja la Harimu 1,017.
Zidzukulu za Harimu 1,017.
wachitatu Harimu, wachinai Seorimu,
Ndi a ana a Harimu: Eliyezere, Isiya, Malikiya, Semaya, Simeoni,
Ana a Pasuri, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi anai ndi asanu ndi awiri.
A Levi: ana a Yesuwa, a Kadimiyele, a ana a Hodeva, makumi asanu ndi awiri kudza anai.