Nehemiya 7:41 - Buku Lopatulika Ana a Pasuri, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi anai ndi asanu ndi awiri. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ana a Pasuri, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi anai ndi asanu ndi awiri. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa A banja la Pasuri 1,247. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Zidzukulu za Pasi-Huri 1,247 |
ndi Adaya mwana wa Yerohamu, mwana wa Pasuri, mwana wa Malikiya, ndi Maasai mwana wa Adiyele, mwana wa Yazera, mwana wa Mesulamu, mwana wa Mesilemiti, mwana wa Imeri,
Ana a Pasuri, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi anai ndi asanu ndi awiri.