Nehemiya 7:40 - Buku Lopatulika Ana a Imeri, chikwi chimodzi mphambu makumi asanu kudza awiri. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ana a Imeri, chikwi chimodzi mphambu makumi asanu kudza awiri. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa A banja la Imara 1,052. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Zidzukulu za Imeri 1,052 |
Potsatizana nao anakonza Zadoki mwana wa Imeri pandunji pa nyumba yake. Ndi potsatizana naye anakonza Semaya mwana wa Sekaniya, wosunga Chipata cha Kum'mawa.
Ansembe: ana a Yedaya, a nyumba ya Yesuwa, mazana asanu ndi anai mphambu makumi asanu ndi awiri kudza atatu.
Ana a Pasuri, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi anai ndi asanu ndi awiri.