Ana a Yeriko, mazana atatu mphambu makumi anai kudza asanu.
A ku Yeriko 345.
Zidzukulu za Yeriko 345
Ndi pambali pake anamanga amuna a ku Yeriko. Ndi pambali pao anamanga Zakuri mwana wa Imuri.
Ana a Harimu, mazana atatu mphambu makumi awiri.
Ana a Lodi, Hadidi, ndi Ono, mazana asanu ndi awiri mphambu makumi awiri kudza mmodzi.