Ana a Elamu winayo, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri ndi makumi asanu kudza anai.
A banja la Elamu wina 1,254.
Ana a Elamu wina 1,254
Ana a Elamu wina, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi asanu ndi anai.
Ana a Elamu, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri ndi makumi asanu kudza anai.
Amuna a ku Nebo winayo, makumi asanu kudza awiri.
Ana a Harimu, mazana atatu mphambu makumi awiri.