Nehemiya 7:32 - Buku Lopatulika Amuna a ku Betele ndi Ai, zana limodzi mphambu makumi awiri kudza atatu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Amuna a ku Betele ndi Ai, zana limodzi mphambu makumi awiri kudza atatu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Amuna a ku Betele ndi Ai 123. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anthu a ku Beteli ndi Ai 123 |
Ana a Benjamini omwe, kuyambira ku Geba pa Mikimasi, ndi Aya, ndi pa Betele ndi midzi yake,
Ndipo sanatsale mwamuna mmodzi yense mu Ai kapena mu Betele osatulukira kwa Israele; nasiya mzinda wapululu, napirikitsa Israele.
Ndipo Yoswa anawatuma, namuka iwo kulowa m'molalira, nakhala pakati pa Betele ndi Ai, kumadzulo kwa Ai; koma Yoswa anakhala mwa anthu usiku uja.