Nehemiya 7:31 - Buku Lopatulika Amuna a ku Mikimasi, zana limodzi mphambu makumi awiri kudza awiri. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Amuna a ku Mikimasi, zana limodzi mphambu makumi awiri kudza awiri. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Amuna a ku Mikimasi 122. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anthu a ku Mikimasi 122 |
Ndipo Afilisti anasonkhana kuti akamenyane ndi Aisraele, anali nao magaleta zikwi makumi atatu, ndi apakavalo zikwi zisanu ndi chimodzi, ndi anthu akuchuluka monga mchenga wa m'mphepete mwa nyanja. Iwowa anakwera namanga zithando ku Mikimasi kum'mawa kwa Betaveni.