Nehemiya 7:30 - Buku Lopatulika Amuna a ku Rama ndi Geba, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi awiri kudza mmodzi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Amuna a ku Rama ndi Geba, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi awiri kudza mmodzi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Amuna a ku Rama ndi Geba, 621. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anthu a ku Rama ndi Geba 621 |
Ana a Benjamini omwe, kuyambira ku Geba pa Mikimasi, ndi Aya, ndi pa Betele ndi midzi yake,
ndi ku Betegiligala, ndi ku minda ya Geba ndi Azimaveti; popeza oimbirawo adadzimangira midzi pozungulira Yerusalemu.
Amuna a ku Kiriyati-Yearimu, Kefira, ndi Beeroti, mazana asanu ndi awiri mphambu makumi anai kudza atatu.