Ana a Kiriyati-Arimu, Kefira, ndi Beeroti, mazana asanu ndi awiri mphambu makumi anai kudza atatu.
Nehemiya 7:29 - Buku Lopatulika Amuna a ku Kiriyati-Yearimu, Kefira, ndi Beeroti, mazana asanu ndi awiri mphambu makumi anai kudza atatu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Amuna a ku Kiriyati-Yearimu, Kefira, ndi Beeroti, mazana asanu ndi awiri mphambu makumi anai kudza atatu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Amuna a ku Kiriyati-Yearimu, Kefira, ndi Beeroti 743. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anthu a ku Kiriati Yeyarimu Kefira ndi Beeroti 743 |
Ana a Kiriyati-Arimu, Kefira, ndi Beeroti, mazana asanu ndi awiri mphambu makumi anai kudza atatu.
Ndipo ana a Israele anayenda ulendo, nafika kumizinda yao tsiku lachitatu. Koma mizinda yao ndiyo Gibiyoni, ndi Kefira, ndi Beeroti ndi Kiriyati-Yearimu.
Nakwera namanga misasa mu Kiriyati-Yearimu, mu Yuda; chifukwa chake anatcha dzina lake la malowo chigono cha Dani, mpaka lero; taona, ali m'tseri mwa Kiriyati-Yearimu.