Nehemiya 7:27 - Buku Lopatulika Amuna a ku Anatoti, zana limodzi mphambu makumi awiri kudza asanu ndi atatu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Amuna a ku Anatoti, zana limodzi mphambu makumi awiri kudza asanu ndi atatu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Amuna a ku Anatoti 128. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anthu a ku Anatoti 128 |
Amuna a ku Betelehemu ndi ku Netofa, zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu kudza asanu ndi atatu.
Mau a Yeremiya mwana wa Hilikiya, wa ansembe amene anali ku Anatoti m'dziko la Benjamini;
Chifukwa chake atero Yehova za anthu a Anatoti, amene afuna moyo wanga, kuti, Usanenere m'dzina la Yehova, ungafe ndi mkono wathu;