Nehemiya 7:26 - Buku Lopatulika Amuna a ku Betelehemu ndi ku Netofa, zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu kudza asanu ndi atatu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Amuna a ku Betelehemu ndi ku Netofa, zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu kudza asanu ndi atatu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Amuna a ku Betelehemu ndi a ku Netofa 188. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anthu a ku Betelehemu ndi Netofa 188 |
Ana a oimbirawo anasonkhana ochokera ku dziko lozungulira Yerusalemu, ndi kumidzi ya Anetofa,
pamenepo anadza kwa Gedaliya ku Mizipa, Ismaele mwana wa Netaniya, ndi Yohanani ndi Yonatani ana a Kareya, ndi Seraya mwana wa Tanumeti, ndi ana a Efayi wa ku Netofa, ndi Yezaniya mwana wa munthu wa ku Maaka, iwo ndi anthu ao.