Ana a Gibiyoni, makumi asanu ndi anai kudza asanu.
A banja la Gibiyoni 95.
Zidzukulu za Gibiyoni 95.
Ana a Gibara, makumi asanu ndi anai mphambu asanu.
Ana a Harifi, zana limodzi mphambu khumi ndi awiri.
Amuna a ku Betelehemu ndi ku Netofa, zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu kudza asanu ndi atatu.