Ana a Harifi, zana limodzi mphambu khumi ndi awiri.
A banja la Harifi 112.
Zidzukulu za Harifu 112
Ana a Yora, zana limodzi mphambu khumi ndi awiri.
Ana a Bezai, mazana atatu mphambu makumi awiri kudza anai.
Ana a Gibiyoni, makumi asanu ndi anai kudza asanu.