Ana a Bezai, mazana atatu mphambu makumi awiri kudza anai.
A banja la Bezai 324.
Zidzukulu za Bezayi 324
Ana a Bezai, mazana atatu mphambu makumi awiri kudza atatu.
Ana a Hasumu, mazana atatu mphambu makumi awiri kudza asanu ndi atatu.
Ana a Harifi, zana limodzi mphambu khumi ndi awiri.