Ana a Atere, a Hezekiya, makumi asanu ndi anai kudza asanu ndi atatu.
A banja la Atere, ndiye kuti la Hezekiya, 98.
Zidzukulu za Ateri (kudzera mwa Hezekiya) 98
Ana a Atere, a Hezekiya, makumi asanu ndi anai mphambu asanu ndi atatu.
Ana a Adini, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu kudza asanu.
Ana a Hasumu, mazana atatu mphambu makumi awiri kudza asanu ndi atatu.