Ana a Adini, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu kudza asanu.
A banja la Adini 655.
Zidzukulu za Adini 655
Ana a Adini, mazana anai mphambu makumi asanu kudza anai.
Ndi wa ana a Adini, Ebedi mwana wa Yonatani; ndi pamodzi naye amuna makumi asanu.
Ana a Bigivai, zikwi ziwiri mphambu makumi asanu ndi limodzi kudza asanu ndi awiri.
Ana a Atere, a Hezekiya, makumi asanu ndi anai kudza asanu ndi atatu.