Ana a Bigivai, zikwi ziwiri mphambu makumi asanu ndi limodzi kudza asanu ndi awiri.
A banja la Bigivai 2,067.
Zidzukulu za Abigivai 2,067
Ana a Bigivai, zikwi ziwiri mphambu makumi asanu kudza asanu ndi mmodzi.
Ana a Adonikamu, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi limodzi, kudza asanu ndi awiri.
Ana a Adini, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu kudza asanu.