Ana a Azigadi, zikwi ziwiri mphambu mazana atatu kudza makumi awiri ndi awiri.
A banja la Azigadi 2,322.
Zidzukulu za Azigadi 2,322
Ana a Azigadi, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi awiri ndi awiri.
Ana a Bebai, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi awiri kudza asanu ndi atatu.
Ana a Adonikamu, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi limodzi, kudza asanu ndi awiri.