Ana a Zakai, mazana asanu ndi awiri mphambu makumi asanu ndi limodzi.
A banja la Zakai 760.
Zidzukulu za Zakai 760
Ana a Zatu, mazana asanu ndi atatu mphambu makumi anai kudza asanu.
Ana a Binuyi, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi anai kudza asanu ndi atatu.