Ana a Zatu, mazana asanu ndi atatu mphambu makumi anai kudza asanu.
A banja la Zatu 845.
Zidzukulu za Zatu 845
Ndi a ana a Zatu: Eliyoenai, Eliyasibu, Mataniya, ndi Yeremoti, ndi Zabadi, ndi Aziza.
Ana a Zatu, mazana asanu ndi anai mphambu makumi anai kudza asanu.
Ana a Elamu, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri ndi makumi asanu kudza anai.
Ana a Zakai, mazana asanu ndi awiri mphambu makumi asanu ndi limodzi.