ndi omanga linga aliyense anamangirira lupanga lake m'chuuno mwake, nagwira ntchito motero. Ndipo woomba lipenga anali ndi ine.
Nehemiya 4:19 - Buku Lopatulika Ndipo ndinati kwa aufulu, ndi olamulira, ndi anthu otsala, Ntchito ndiyo yochuluka ndi yachitando, ndi ife tili palakepalake palingapo, yense atalikizana ndi mnzake; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ndinati kwa aufulu, ndi olamulira, ndi anthu otsala, Ntchito ndiyo yochuluka ndi yachitando, ndi ife tili palakepalake palingapo, yense atalikizana ndi mnzake; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndidaŵauza atsogoleri ndi akuluakulu ndiponso anthu ena onse aja kuti, “Ntchitoyi njaikulu, ili pa dera lalikulu, ndipo ifeyo takhala motayanatayana kwambiri pa khoma. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo ine ndinati kwa anthu olemekezeka ndi anthu ena onse, “Ntchitoyi ndi yayikulu ndipo ili padera lalikulu ndipo ifeyo takhala motayanatayana kwambiri pa khoma. |
ndi omanga linga aliyense anamangirira lupanga lake m'chuuno mwake, nagwira ntchito motero. Ndipo woomba lipenga anali ndi ine.
paliponse mukumva mau a lipenga, musonkhanire komweko kwa ife; Mulungu wathu adzatigwirira nkhondo.