Ndipo panali ngati mapewa anai pansi pangodya zinali za phaka limodzi, mapewawo anali a phaka lomwelo.
Nehemiya 3:27 - Buku Lopatulika Potsatizana nao Atekowa anakonza gawo lina, pandunji pa nsanja yaikulu yosomphoka ndi kulinga la Ofele. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Potsatizana nao Atekowa anakonza gawo lina, pandunji pa nsanja yaikulu yosomphoka ndi kulinga la Ofele. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pambali pa Pedaya ndi anzake, Atekowa adakonza chigawo china choyang'anana ndi nsanja ija yaikulu ndi yaitali mpaka kukafika ku khoma la Ofele. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Motsatana nawo, anthu a ku Tekowa anakonzanso chigawo china choyangʼanana ndi nsanja ija yayikulu ndi yayitali mpaka ku khoma la Ofeli. |
Ndipo panali ngati mapewa anai pansi pangodya zinali za phaka limodzi, mapewawo anali a phaka lomwelo.
Ndi pambali pao anakonza Atekowa; koma omveka ao sanapereke makosi ao kuntchito ya Mbuye wao.