Ana a oimbirawo anasonkhana ochokera ku dziko lozungulira Yerusalemu, ndi kumidzi ya Anetofa,
Nehemiya 3:22 - Buku Lopatulika Ndi potsatizana naye anakonza ansembe okhala kuchidikha. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi potsatizana naye anakonza ansembe okhala kuchidikha. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pambali pa Meremoti, ansembe okhala ku chidikha adakonza chigawo china. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pambuyo pake ansembe okhala ku chidikha anakonzanso chigawo china. |
Ana a oimbirawo anasonkhana ochokera ku dziko lozungulira Yerusalemu, ndi kumidzi ya Anetofa,
Potsatizana naye Meremoti mwana wa Uriya mwana wa Hakozi anakonza gawo lina, kuyambira kukhomo la nyumba ya Eliyasibu kufikira malekezero ake a nyumba ya Eliyasibu.
Potsatizana nao anakonza Benjamini ndi Hasubu pandunji pa nyumba pao. Potsatizana nao anakonza Azariya mwana wa Maaseiya mwana wa Ananiya pafupi pa nyumba yake.
anatumiza mau kwa ine Sanibalati ndi Gesemu, kuti, Tiyeni tikomane kumidzi ya ku Chigwa cha Ono; koma analingirira za kundichitira choipa.