Ndi ana a Hananiya: Pelatiya, ndi Yesaya, ana a Refaya, ana a Arinani, ana a Obadiya, ana a Sekaniya.
Nehemiya 12:3 - Buku Lopatulika Sekaniya, Rehumu, Meremoti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Sekaniya, Rehumu, Meremoti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Sekaniya, Rehumu, Meremoti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Sekaniya, Rehumu, Meremoti, |
Ndi ana a Hananiya: Pelatiya, ndi Yesaya, ana a Refaya, ana a Arinani, ana a Obadiya, ana a Sekaniya.
Potsatizana naye anakonza Alevi, Rehumu mwana wa Bani. Pambali pake anakonza Hasabiya mkulu wa dera lina la dziko la Keila, kukonzera dziko lake.
ndiwo amene anadza ndi Zerubabele: Yesuwa, Nehemiya, Azariya, Raamiya, Nahamani, Mordekai, Bilisani, Misipereti, Bigivai, Nehumu, Baana. Mawerengedwe a amuna a anthu Aisraele ndiwo: