Ndipo m'mene adaitana mfumu, anawatulukira Eliyakimu mwana wa Hilikiya woyang'anira nyumba ya mfumu, ndi Sebina mlembi, ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba mbiri.
Nehemiya 12:21 - Buku Lopatulika wa Hilikiya, Hasabiya; wa Yedaya, Netanele. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 wa Hilikiya, Hasabiya; wa Yedaya, Netanele. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Wa fuko la Hilikiya anali Hasabiya ndipo wa fuko la Yedaya anali Netanele. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero wa fuko la Hilikiya anali Hasabiya; wa fuko la Yedaya anali Netaneli. |
Ndipo m'mene adaitana mfumu, anawatulukira Eliyakimu mwana wa Hilikiya woyang'anira nyumba ya mfumu, ndi Sebina mlembi, ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba mbiri.
M'masiku a Eliyasibu, Yoyada, Yohanani, ndi Yaduwa, Alevi analembedwa akulu a nyumba za makolo; ansembe omwe, mpaka ufumu wa Dariusi wa ku Persiya.