Nehemiya 12:13 - Buku Lopatulika wa Ezara, Mesulamu; wa Amariya, Yehohanani; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 wa Ezara, Mesulamu; wa Amariya, Yehohanani; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Wa fuko la Ezara anali Mesulamu, wa fuko la Amariya anali Yehohanani. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero wa fuko la Ezara anali Mesulamu; wa fuko la Amariya anali Yehohanani; |
Ndi m'masiku a Yoyakimu ansembe aakulu a nyumba za makolo ndiwo: wa Seraya, Meraya; wa Yeremiya, Hananiya;
Ndipo Ezara mlembi anaima pa chiunda cha mitengo adachimangira msonkhanowo; ndi pambali pake padaima Matitiya, ndi Sema, ndi Anaya, ndi Uriya, ndi Hilikiya, ndi Maaseiya, kudzanja lamanja lake; ndi kudzanja lamanzere Pedaya, ndi Misaele, ndi Malikiya, ndi Hasumu, ndi Hasibadana, Zekariya, ndi Mesulamu.