Ndi Yesuwa anabala Yoyakimu, ndi Yoyakimu anabala Eliyasibu ndi Eliyasibu anabala Yoyada,
Nehemiya 12:11 - Buku Lopatulika ndi Yoyada anabala Yonatani, ndi Yonatani, anabala Yaduwa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi Yoyada anabala Yonatani, ndi Yonatani, anabala Yaduwa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yoyada adabereka Yonatani ndipo Yonatani adabereka Yaduwa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yoyada anabereka Yonatani, ndipo Yonatani anabereka Yaduwa. |
Ndi Yesuwa anabala Yoyakimu, ndi Yoyakimu anabala Eliyasibu ndi Eliyasibu anabala Yoyada,
Ndi m'masiku a Yoyakimu ansembe aakulu a nyumba za makolo ndiwo: wa Seraya, Meraya; wa Yeremiya, Hananiya;
M'masiku a Eliyasibu, Yoyada, Yohanani, ndi Yaduwa, Alevi analembedwa akulu a nyumba za makolo; ansembe omwe, mpaka ufumu wa Dariusi wa ku Persiya.