Nehemiya 10:8 - Buku Lopatulika Maaziya, Biligai, Semaya, ndiwo ansembe. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Maaziya, Biligai, Semaya, ndiwo ansembe. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Maziya, Biligai ndi Semaya. Ameneŵa ndiwo anali ansembe. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Maziya, Biligai ndi Semaya Awa anali ansembe. |
ndi Maaseiya, ndi Semaya, ndi Eleazara, ndi Uzi, ndi Yehohanani, ndi Malikiya, ndi Elamu, ndi Ezere. Ndipo oimbira anaimbitsa Yezeraya ndiye woyang'anira wao.
Potsatizana nao anakonza Zadoki mwana wa Imeri pandunji pa nyumba yake. Ndi potsatizana naye anakonza Semaya mwana wa Sekaniya, wosunga Chipata cha Kum'mawa.