Ndi ana a mkazi wa Hodiya, mlongo wake wa Nahamu, ndiwo atate a Keila Mgarimi ndi Esitemowa Mmaaka.
Nehemiya 10:13 - Buku Lopatulika Hodiya, Bani, Beninu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Hodiya, Bani, Beninu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Hodiya, Bani ndi Benimu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Hodiya, Bani ndi Beninu. |
Ndi ana a mkazi wa Hodiya, mlongo wake wa Nahamu, ndiwo atate a Keila Mgarimi ndi Esitemowa Mmaaka.
Utai mwana wa Amihudi, mwana wa Omuri, mwana wa Imuri, mwana wa Bani, wa ana a Perezi mwana wa Yuda.
Ndipo woyang'anira wa Alevi mu Yerusalemu ndiye Uzi mwana wa Bani, mwana wa Hasabiya, mwana wa Mataniya, mwana wa Mika; mwa ana a Asafu oimbira ena anayang'anira ntchito ya m'nyumba ya Mulungu.