Nehemiya 10:12 - Buku Lopatulika Zakuri, Serebiya, Sebaniya, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Zakuri, Serebiya, Sebaniya, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Zakuri, Serebiya, Sebaniya, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Zakuri, Serebiya, Sebaniya, |
Ndi Alevi ndiwo Yesuwa, Binuyi, Kadimiyele, Serebiya, Yuda, ndi Mataniya; iye ndi abale ake amatsogolera mayamiko.
Ndi pambali pake anamanga amuna a ku Yeriko. Ndi pambali pao anamanga Zakuri mwana wa Imuri.
Ndi Yesuwa, ndi Bani, ndi Serebiya, Yamini, Akubu, Sabetai, Hodiya, Maaseiya, Kelita, Azariya, Yozabadi, Hanani, Pelaya, ndi Alevi, anadziwitsa anthu chilamulocho; ndi anthu anali chilili pamalo pao.
Pamenepo anaimirira pa chiunda cha Alevi Yesuwa, ndi Bani, Kadimiyele, Sebaniya, Buni, Serebiya, Bani, ndi Kenani, nafuula ndi mau aakulu kwa Yehova Mulungu wao.