Kodi mau ochulukawa sayenera kuwayankha? Ndi munthu wa milomo ayenera kuyesedwa wolungama?
Mlaliki 5:3 - Buku Lopatulika Pakuti loto lafika mwakuchuluka ntchito; ndipo mau a chitsiru mwakuchuluka maneno. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pakuti loto lafika mwakuchuluka ntchito; ndipo mau a chitsiru mwakuchuluka maneno. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kuchuluka kwa mavuto mu mtima kumabweretsa maloto oipa, ndipo kuchuluka kwa mau kumadzetsa uchitsiru. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kuchuluka kwa mavuto mu mtima kumabweretsa maloto oyipa, ndipo kuchuluka kwa mawu kumadzetsa uchitsiru. |
Kodi mau ochulukawa sayenera kuwayankha? Ndi munthu wa milomo ayenera kuyesedwa wolungama?
Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Pamene munthu achita chowinda cha padera, anthuwo azikhala a Yehova monga mwa kuyesa kwako.