Chifukwa chake ndinada moyo; pakuti ntchito azipanga kunja kuno zindisautsa; pakuti zonse ndi chabe ndi kungosautsa mtima.
Mlaliki 4:2 - Buku Lopatulika Ndipo ndinatama akufa atatha kufa kupambana amoyo omwe alipobe; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ndinatama akufa atatha kufa kupambana amoyo omwe alipobe; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndinkaganiza kuti akufa aja amene adapita kale ndi amwai kwambiri kupambana amene akadali ndi moyo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo ndinanena kuti akufa, amene anafa kale, ndi osangalala kuposa amoyo, amene akanalibe ndi moyo. |
Chifukwa chake ndinada moyo; pakuti ntchito azipanga kunja kuno zindisautsa; pakuti zonse ndi chabe ndi kungosautsa mtima.
Musamlirire wakufa, musachite maliro ake; koma mumliritse iye amene amuka, pakuti sadzabweranso, kapena kuonanso dziko la kwao.