Mlaliki 3:9 - Buku Lopatulika Wogwira Ntchito aona phindu lanji m'chomsautsacho? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wogwira Ntchito aona phindu lanji m'chomsautsacho? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kodi wantchito amapeza phindu lanji pa ntchito yake yolemetsa? Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kodi wantchito amapeza phindu lanji pa ntchito yake yolemetsa? |
Pamenepo ndinayang'ana zonse manja anga anazipanga, ndi ntchito zonse ndinasauka pozigwira; ndipo taona, zonse zinali zachabechabe ndi kungosautsa mtima, ndipo kunalibe phindu kunja kuno.
Ichinso ndi choipa chowawa, chakuti adzangopita monse monga anadza; ndipo wodzisautsa chabe adzaona phindu lanji?
Pakuti munthu adzapindulanji, akalandira dziko lonse, nataya moyo wake? Kapena munthu adzaperekanji chosintha ndi moyo wake?